Genesis 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:29 Nsanja ya Olonda,8/1/1989, ptsa. 19-20
29 Tsopano Mulungu anati: “Taonani, ndakupatsani zomera zonse zobala mbewu zapadziko lonse lapansi, ndi mitengo yonse yobala zipatso za mbewu+ kuti zikhale chakudya chanu.+