Yobu 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndi zimenezi, iye amaweruza mokomera mitundu ya anthu.+Amapereka chakudya chochuluka.+ Salimo 145:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mumatambasula dzanja lanu+Ndi kukhutiritsa zokhumba za chamoyo chilichonse.+