Genesis 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ananenanso kuti: “Simunandipatse mbewu+ ndipo mtumiki wanga+ ndiye adzakhale wolowa nyumba yanga.”