Genesis 15:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo iye anauza Abulamu kuti: “Unditengere ng’ombe ya zaka zitatu yomwe sinaberekepo, mbuzi yaikazi ya zaka zitatu, nkhosa yamphongo ya zaka zitatu, ndiponso njiwa yaing’ono ndi mwana wa nkhunda.”+
9 Pamenepo iye anauza Abulamu kuti: “Unditengere ng’ombe ya zaka zitatu yomwe sinaberekepo, mbuzi yaikazi ya zaka zitatu, nkhosa yamphongo ya zaka zitatu, ndiponso njiwa yaing’ono ndi mwana wa nkhunda.”+