-
Genesis 2:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho munthuyo anali kutcha mayina nyama zonse zoweta, ndiponso zolengedwa zonse zouluka m’mlengalenga, komanso nyama iliyonse yakutchire. Koma munthuyo analibe womuthandiza, monga mnzake womuyenerera.
-