23 Chotero lumbira panopo kuti, pali Mulungu+ udzakhala wokhulupirika kwa ine, kwa ana anga ndi kwa mbadwa zanga.+ Ndiponso kuti udzatero chifukwa cha chikondi chosatha+ chimene ine ndakusonyeza. Choncho udzandichitira ine motero, pamodzi ndi dziko limene ukukhalamo monga mlendoli.”+