Ekisodo 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo ana a Isiraeli anachoka ndi kukachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aroni.+ Anachitadi momwemo. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:28 Nsanja ya Olonda,12/15/1995, tsa. 12
28 Pamenepo ana a Isiraeli anachoka ndi kukachita monga momwe Yehova analamulira Mose ndi Aroni.+ Anachitadi momwemo.