Ekisodo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mahatchi a Farao,+ magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi atalowa m’nyanja,+Yehova wabweza madzi a m’nyanjamo ndi kuwamiza.+Koma ana a Isiraeli ayenda panthaka youma pakati pa nyanja.”+
19 Mahatchi a Farao,+ magaleta ake ankhondo ndi asilikali ake apamahatchi atalowa m’nyanja,+Yehova wabweza madzi a m’nyanjamo ndi kuwamiza.+Koma ana a Isiraeli ayenda panthaka youma pakati pa nyanja.”+