Levitiko 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo azizibweretsa kwa wansembe, ndipo wansembeyo azipereka nsembe yamachimo choyamba, ataicheka+ pakhosi koma osaduliratu mutu wake.
8 Pamenepo azizibweretsa kwa wansembe, ndipo wansembeyo azipereka nsembe yamachimo choyamba, ataicheka+ pakhosi koma osaduliratu mutu wake.