-
Levitiko 5:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Azibweretsa kwa wansembe nkhosa yopanda chilema kuti ikhale nsembe ya kupalamula.+ Mtengo wa nkhosayo uzikhala wofanana ndi mtengo wake woikidwiratu. Ndiyeno wansembe aziphimba machimo+ a munthuyo chifukwa cha cholakwa chimene wachita mosadziwa, ngakhale kuti sanazindikire zotsatira zake, ndipo azikhululukidwa.+
-