Levitiko 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Imeneyi ndi nsembe ya kupalamula. Munthu ameneyo wapalamula mlandu+ kwa Yehova.”