Levitiko 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Usatemberere munthu wogontha, ndipo usaikire munthu wakhungu chinthu chopunthwitsa.+ Uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, ptsa. 8-9
14 “‘Usatemberere munthu wogontha, ndipo usaikire munthu wakhungu chinthu chopunthwitsa.+ Uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova.