Levitiko 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamatemberere* munthu amene ali ndi vuto losamva ndipo munthu amene ali ndi vuto losaona musamamuikire chinthu chopunthwitsa.+ Muziopa Mulungu wanu.+ Ine ndine Yehova. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:14 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, ptsa. 8-9
14 Musamatemberere* munthu amene ali ndi vuto losamva ndipo munthu amene ali ndi vuto losaona musamamuikire chinthu chopunthwitsa.+ Muziopa Mulungu wanu.+ Ine ndine Yehova.