Levitiko 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndipo ngati Mlevi anagulitsa nyumba mumzinda wawo ndipo sanaiwombole, izibwezedwa kwa Mleviyo m’Chaka cha Ufulu.+ Zizikhala choncho chifukwa nyumba za m’mizinda ya Alevi pakati pa ana a Isiraeli ndi za Aleviwo basi.+
33 Ndipo ngati Mlevi anagulitsa nyumba mumzinda wawo ndipo sanaiwombole, izibwezedwa kwa Mleviyo m’Chaka cha Ufulu.+ Zizikhala choncho chifukwa nyumba za m’mizinda ya Alevi pakati pa ana a Isiraeli ndi za Aleviwo basi.+