Levitiko 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndipo ngati Mlevi anagulitsa nyumba mumzinda wawo ndipo sanaiwombole, izibwezedwa kwa Mleviyo mʼChaka cha Ufulu.+ Zizikhala choncho chifukwa nyumba zamʼmizinda ya Alevi pakati pa Aisiraeli ndi za Aleviwo basi.+
33 Ndipo ngati Mlevi anagulitsa nyumba mumzinda wawo ndipo sanaiwombole, izibwezedwa kwa Mleviyo mʼChaka cha Ufulu.+ Zizikhala choncho chifukwa nyumba zamʼmizinda ya Alevi pakati pa Aisiraeli ndi za Aleviwo basi.+