Levitiko 25:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 “‘Pakuti kwa ine ana a Isiraeli ndi akapolo. Ndi akapolo anga+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+
55 “‘Pakuti kwa ine ana a Isiraeli ndi akapolo. Ndi akapolo anga+ amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+