-
Levitiko 27:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 “‘Ndiyeno ngati zaka za munthu woperekedwayo ndi zoyambira pa 60 kupita m’tsogolo, akakhala wamwamuna, mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli 15, ndipo akakhala wamkazi ndi masekeli 10.
-