Numeri 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akatero, azitenga ziwiya zonse+ zimene amachitira utumiki wawo nthawi zonse m’malo oyera, n’kuzikuta ndi nsalu yabuluu. Ndiyeno aziziphimba ndi zikopa za akatumbu,+ n’kuikako mtengo wake wonyamulira.
12 Akatero, azitenga ziwiya zonse+ zimene amachitira utumiki wawo nthawi zonse m’malo oyera, n’kuzikuta ndi nsalu yabuluu. Ndiyeno aziziphimba ndi zikopa za akatumbu,+ n’kuikako mtengo wake wonyamulira.