Numeri 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akatero, azitenga ziwiya zonse+ zimene amagwiritsa ntchito pa utumiki wawo nthawi zonse mʼmalo oyera, nʼkuzikuta ndi nsalu yabuluu. Ndiyeno aziziphimba ndi zikopa za akatumbu, nʼkuziika pandodo yonyamulira.
12 Akatero, azitenga ziwiya zonse+ zimene amagwiritsa ntchito pa utumiki wawo nthawi zonse mʼmalo oyera, nʼkuzikuta ndi nsalu yabuluu. Ndiyeno aziziphimba ndi zikopa za akatumbu, nʼkuziika pandodo yonyamulira.