Numeri 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno Yehova anamuyankha Mose kuti: “Kodi dzanja la Yehova lafupika lero eti?+ Tsopano uona ngati zimene ndanena zichitikedi kapena ayi.”+
23 Ndiyeno Yehova anamuyankha Mose kuti: “Kodi dzanja la Yehova lafupika lero eti?+ Tsopano uona ngati zimene ndanena zichitikedi kapena ayi.”+