Numeri 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Iwe udzakhala wopanda cholowa m’dziko mwawo, ndipo sudzapatsidwa gawo lililonse pakati pawo.+ Ine ndine gawo lako ndi cholowa chako pakati pa ana a Isiraeli.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:20 Nsanja ya Olonda,12/15/2011, tsa. 319/15/2011, ptsa. 7-84/15/1998, tsa. 20
20 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Aroni, kuti: “Iwe udzakhala wopanda cholowa m’dziko mwawo, ndipo sudzapatsidwa gawo lililonse pakati pawo.+ Ine ndine gawo lako ndi cholowa chako pakati pa ana a Isiraeli.+