Numeri 21:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa nthawi imeneyo Aisiraeli anaimba nyimbo+ yakuti:“Tumphuka, chitsime iwe! Vomerezani nyimboyo, anthu inu!
17 Pa nthawi imeneyo Aisiraeli anaimba nyimbo+ yakuti:“Tumphuka, chitsime iwe! Vomerezani nyimboyo, anthu inu!