Numeri 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chitsimechi n’chokumbidwa ndi akalonga. Chofukula anthu olemekezeka,Chofukula ndi ndodo ya mtsogoleri wa asilikali,+ chofukula ndi ndodo zawo.” Atachoka kuchipululucho anafika ku Matana.
18 Chitsimechi n’chokumbidwa ndi akalonga. Chofukula anthu olemekezeka,Chofukula ndi ndodo ya mtsogoleri wa asilikali,+ chofukula ndi ndodo zawo.” Atachoka kuchipululucho anafika ku Matana.