Numeri 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atachoka ku Bamoti anafika kuchigwa cha dziko la Mowabu,+ kumalire ndi mzinda wa Pisiga.+ Chitunda cha Pisiga chinayang’anana ndi dera la Yesimoni.+
20 Atachoka ku Bamoti anafika kuchigwa cha dziko la Mowabu,+ kumalire ndi mzinda wa Pisiga.+ Chitunda cha Pisiga chinayang’anana ndi dera la Yesimoni.+