Numeri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tiloleni tidzere m’dziko lanu. Sitipatukira pamunda uliwonse, kapena pamunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mumsewu wa mfumu mpaka titadutsa m’dziko lanu.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:22 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 8-9
22 “Tiloleni tidzere m’dziko lanu. Sitipatukira pamunda uliwonse, kapena pamunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mumsewu wa mfumu mpaka titadutsa m’dziko lanu.”+