Numeri 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti pomwe ndili pano ndikutha kuwaona, pamwamba pa matanthwe pano,Ndikuwaona ndithu, pano pamwamba pa mapiri.Akukhala paokhaokha m’mahema awo,+Iwo akudziona kuti ndi osiyana ndi mitundu ina.+
9 Pakuti pomwe ndili pano ndikutha kuwaona, pamwamba pa matanthwe pano,Ndikuwaona ndithu, pano pamwamba pa mapiri.Akukhala paokhaokha m’mahema awo,+Iwo akudziona kuti ndi osiyana ndi mitundu ina.+