Numeri 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 bambo ake n’kumumva ndithu akulonjeza kapena akuchita lonjezo lodzimanalo,+ koma osanenapo kanthu, malonjezo ake onsewo akhale momwemo. Zikatero, lonjezo lake lililonse lodzimana likhale momwemo.
4 bambo ake n’kumumva ndithu akulonjeza kapena akuchita lonjezo lodzimanalo,+ koma osanenapo kanthu, malonjezo ake onsewo akhale momwemo. Zikatero, lonjezo lake lililonse lodzimana likhale momwemo.