Deuteronomo 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zisakhale zovuta kwa iwe kum’masula kuti achoke,+ chifukwa wakutumikira zaka 6, moti malipiro ake akanafanana ndi malipiro a anthu awiri aganyu,+ ndipo Yehova Mulungu wako wakudalitsa pa chilichonse chimene wachita.+
18 Zisakhale zovuta kwa iwe kum’masula kuti achoke,+ chifukwa wakutumikira zaka 6, moti malipiro ake akanafanana ndi malipiro a anthu awiri aganyu,+ ndipo Yehova Mulungu wako wakudalitsa pa chilichonse chimene wachita.+