-
Deuteronomo 30:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiponso silili tsidya lina la nyanja kuti unene kuti, ‘Ndani adzawoloka kupita tsidya lina la nyanja kukatitengera lamulolo kuti ife tilimve ndi kulitsatira?’
-