Deuteronomo 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+Mawu anga adzatsika ngati mame,+Ngati mvula yowaza pa udzu,+Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2020, tsa. 10 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2016, ptsa. 3-4
2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+Mawu anga adzatsika ngati mame,+Ngati mvula yowaza pa udzu,+Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+