Deuteronomo 32:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:5 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 10
5 Iwo achita okha zinthu zowawonongetsa,+Si ana ake, chilemacho n’chawo.+Iwo ndiwo m’badwo wopotoka maganizo ndi wokhotakhota!+