Deuteronomo 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:6 Nsanja ya Olonda,9/1/2008, tsa. 5
6 Kodi mukupitiriza kuchitira Yehova mwa njira imeneyi,+Anthu opusa ndi opanda nzeru inu?+Kodi iye si Atate wanu amene anakulengani,+Amene anakupangani ndi kukuchititsani kukhazikika?+