Deuteronomo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani masiku akale,+Ganizirani zaka za mibadwomibadwo ya m’mbuyomu.Funsa bambo ako ndipo akuuza,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozera.+
7 Kumbukirani masiku akale,+Ganizirani zaka za mibadwomibadwo ya m’mbuyomu.Funsa bambo ako ndipo akuuza,+Amuna achikulire pakati panu, ndipo akufotokozera.+