Deuteronomo 32:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+
25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+