Deuteronomo 32:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Pakuti amenewa si mawu opanda pake kwa inu,+ chifukwa mawu amenewa ndiwo moyo wanu.+ Mwa kutsatira mawu amenewa mudzatalikitsa masiku anu panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu, mutawoloka Yorodano.”+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:47 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2023, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,4/15/2008, ptsa. 5-6
47 Pakuti amenewa si mawu opanda pake kwa inu,+ chifukwa mawu amenewa ndiwo moyo wanu.+ Mwa kutsatira mawu amenewa mudzatalikitsa masiku anu panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu, mutawoloka Yorodano.”+