1 Samueli 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Elikana anali ndi akazi awiri. Mkazi wina dzina lake anali Hana ndipo wina anali Penina. Penina anabereka ana koma Hana analibe ana.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:2 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 15
2 Elikana anali ndi akazi awiri. Mkazi wina dzina lake anali Hana ndipo wina anali Penina. Penina anabereka ana koma Hana analibe ana.+