1 Samueli 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 15
9 Pamenepo Hana anaimirira atadya ndi kumwa ku Silo. Apa n’kuti Eli wansembe atakhala pampando, pakhomo la kachisi+ wa Yehova.