1 Samueli 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hana anali wokhumudwa kwabasi,+ ndipo anayamba kupemphera kwa Yehova+ ndi kulira kwambiri.+