1 Samueli 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Eli anamuuza kuti: “Kodi ukhala woledzera mpaka liti?+ Pita kaye, kuledzera kwakoku kuyambe kwatha.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:14 Tsanzirani, tsa. 55 Nsanja ya Olonda,7/1/2010, tsa. 162/1/2001, tsa. 20
14 Choncho Eli anamuuza kuti: “Kodi ukhala woledzera mpaka liti?+ Pita kaye, kuledzera kwakoku kuyambe kwatha.”