1 Samueli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamenepo Eli anamuyankha kuti: “Pita mu mtendere,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli akupatse zimene wam’pempha.”+
17 Pamenepo Eli anamuyankha kuti: “Pita mu mtendere,+ ndipo Mulungu wa Isiraeli akupatse zimene wam’pempha.”+