1 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene anali okhuta ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,+Koma anjala, njala yawo yawathera.+ Ngakhale wosabereka, wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, wasiya kubereka.+
5 Amene anali okhuta ayenera kugwira ganyu kuti apeze chakudya,+Koma anjala, njala yawo yawathera.+ Ngakhale wosabereka, wabereka ana 7,+Koma amene anali ndi ana aamuna ambiri, wasiya kubereka.+