1 Samueli 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense akamapereka nsembe ankayeneranso kupereka gawo la nyamayo kwa wansembe.+ Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, pamene nyama imeneyi inali kuwira, mtumiki wa wansembe anali kubwera ndi foloko ya mano atatu m’manja mwake.+
13 Munthu aliyense akamapereka nsembe ankayeneranso kupereka gawo la nyamayo kwa wansembe.+ Ndiyeno zimene zinali kuchitika n’zakuti, pamene nyama imeneyi inali kuwira, mtumiki wa wansembe anali kubwera ndi foloko ya mano atatu m’manja mwake.+