1 Samueli 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 ndipo Yehova anakomera mtima Hana,+ moti anayamba kutenga pakati ndipo anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri.+ Mwanayo Samueli anapitiriza kukula, akukondedwa ndi Yehova.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:21 Tsanzirani, tsa. 63 Nsanja ya Olonda,10/1/2010, tsa. 16
21 ndipo Yehova anakomera mtima Hana,+ moti anayamba kutenga pakati ndipo anabereka ana aamuna atatu ndi aakazi awiri.+ Mwanayo Samueli anapitiriza kukula, akukondedwa ndi Yehova.+