-
1 Samueli 2:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 “‘N’chifukwa chake Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Ndinanenadi kuti, A m’nyumba yako ndiponso a m’nyumba ya kholo lako adzanditumikira mpaka kalekale.”+ Koma tsopano Yehova akuti: “Sindingachitenso zimenezo, chifukwa amene akundilemekeza+ ndiwalemekeza,+ koma amene akundinyoza ndi opanda pake kwa ine.”+
-