1 Samueli 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Sauli anatuma amithenga kuti akagwire Davide, koma Mikala anati: “Akudwala.”+