1 Mafumu 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Solomo anaiyankha mfumukaziyo mafunso ake onse.+ Panalibe chimene mfumuyo inalephera kuyankha.+