1 Mafumu 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamasitepe 6 amenewo, panali zifaniziro 12 za mikango itaimirira, mbali iyi ndi iyi. Panalibenso ufumu wina umene unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.+
20 Pamasitepe 6 amenewo, panali zifaniziro 12 za mikango itaimirira, mbali iyi ndi iyi. Panalibenso ufumu wina umene unali ndi mpando wachifumu ngati umenewo.+