Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 23:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Atafika anaona mfumu itaimirira pafupi ndi chipilala chake+ pakhomo. Anaonanso akalonga+ ndi anthu oimba malipenga+ ali pafupi ndi mfumuyo, ndipo anthu onse a m’dzikolo anali kusangalala+ ndi kuimba+ malipenga. Panalinso oimba+ ndi zipangizo zoimbira ndiponso anthu otsogolera poimba nyimbo zotamanda. Nthawi yomweyo Ataliya anang’amba zovala zake n’kuyamba kunena kuti: “Mwandichitira chiwembu! Mwandichitira chiwembu!”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena