Nehemiya 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano amuna ena pamodzi ndi akazi awo anayamba kudandaula kwambiri+ ndipo anali kutsutsana ndi abale awo achiyuda.+
5 Tsopano amuna ena pamodzi ndi akazi awo anayamba kudandaula kwambiri+ ndipo anali kutsutsana ndi abale awo achiyuda.+