Nehemiya 12:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Maaseya, Semaya, Eleazara, Uzi, Yehohanani, Malikiya, Elamu ndi Ezeri. Ndipo oimba pamodzi ndi Izirahiya woyang’anira wawo anali kuimba mokweza.+
42 Maaseya, Semaya, Eleazara, Uzi, Yehohanani, Malikiya, Elamu ndi Ezeri. Ndipo oimba pamodzi ndi Izirahiya woyang’anira wawo anali kuimba mokweza.+